Numeri 26:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi.

Numeri 26

Numeri 26:33-46