Numeri 26:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo ndiwo mabanja a ana a Efraimu monga mwa owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana asanu. Iwo ndiwo ana amuna a Yosefe monga mwa mabanja ao.

Numeri 26

Numeri 26:29-47