Numeri 25:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Sautsa Amidyani ndi kuwakantha;

18. popeza akusautsani ndi manyengo ao amene anakunyengani nao; m'cija ca Peori, ndi ca Kozibi, mwana wamkazi wa kalonga wa ku Midyani, mlongo wao, amene adamupha tsiku la mliri, m'cija ca Peori.

Numeri 25