Numeri 25:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo lidzakhala kwa iye, ndi kwa mbeu zace zakumtsata pangano la unsembe wosatha, popeza anacita nsanje cifukwa ca Mulungu wace, anawacitira ana a Israyeli cowatetezera.

Numeri 25

Numeri 25:4-17