Numeri 24:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anaunthama, nagona pansi ngati mkango,Ngati mkango waukazi; adzamuutsa ndani?Wodalitsika ali yense wakudalitsa iwe,Wotemberereka ali yense wakutemberera iwe.

Numeri 24

Numeri 24:4-16