Numeri 24:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ziyalika monga zigwa,Monga minda m'mphepete mwanyanja,Monga khonje waoka Yehova,Monga mikungudza m'mphepete mwa madzi.

Numeri 24

Numeri 24:1-8