Numeri 24:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayang'ana ku Amaleki, nanena fanizo lace, nati,Amaleki ndiye woyamba wa amitundu;Koma citsiriziro cace, adzaonongeka ku nthawi zonse.

Numeri 24

Numeri 24:15-23