Numeri 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Balamu anaona kuti kudakomera pamaso pa Yehova kudalitsa Israyeli, sanamuka, monga nthawi zija zina, ku nyanga zolodzera, koma anayang'ana nkhope yace kucipululu.

Numeri 24

Numeri 24:1-6