Numeri 23:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Mundimangire pano maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere pano ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.

Numeri 23

Numeri 23:20-30