Numeri 23:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza kuli iye, ndipo taona, analikuima pa nsembe yace yopsereza, ndi akalonga a Moabu pamodzi naye. Ndipo Balaki anati kwa iye, Wanenanji Yehova?

Numeri 23

Numeri 23:8-18