Numeri 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzawerenga ndani pfumbi la Yakobo,Kapena kuwerenga limodzi la magawo anai la Israyeli?Ndipo ine ndife monga amafa aongoka mtima,Citsiriziro canga cifanane naco cace!

Numeri 23

Numeri 23:6-19