Numeri 22:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru a Moabu ndi akuru a Midyani anamuka ndi mphotho za maula m'dzanja lao; anadza kwa Balamu, nanena naye mau a Balaki.

Numeri 22

Numeri 22:6-14