Numeri 22:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Balamu anati kwa buru, Cifukwa wandipeputsa; mukadakhala lupanga m'dzanja langa tsopano, ndikadakupha iwe.

Numeri 22

Numeri 22:20-36