Numeri 21:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Hesiboni ndiwo mudzi wa Sihoni mfumu ya Aamori, imene idathira nkhondo pa mfumu idafayo ya Moabu, nilanda dziko lace m'dzanja lace kufikira Arinoni.

Numeri 21

Numeri 21:21-34