Numeri 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atacokako anayenda ulendo, namanga mahema tsidya tina la Arinoni, wokhala m'cipululu, wogwera ku malire a Aamori; popeza Arinoni ndiwo malire a Moabu, pakati pa Moabu ndi Aamori.

Numeri 21

Numeri 21:3-18