Numeri 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Mkanani, mfumu ya Aradi, wokhala kumwela, anamva kuti Israyeli anadzera njira ya azondi, anathira nkhondo pa Israyeli, nagwira ena akhale ansinga.

Numeri 21

Numeri 21:1-8