Numeri 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munatikwezeranji kutiturutsa m'Aigupto, kutilowetsa m'malo oipa ano? Si malo a mbeu awa, kapena mkuyu, kapena mpesa kapena makangaza; ngakhale madzi akumwa palibe.

Numeri 20

Numeri 20:1-6