Numeri 20:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, Popeza simunandikhulupirira Ine, kundipatula Ine pamaso pa ana a Israyeli, cifukwa cace simudzalowetsa msonkhano uwu m'dziko ndinawapatsali.

Numeri 20

Numeri 20:11-19