Numeri 2:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a pfuko la Aseri; ndi kalonga wa ana a Aseri ndiye Pagiyeli mwana wa Okirani.

Numeri 2

Numeri 2:23-33