Numeri 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Owerengedwa onse a cigono ca Efraimu ndiwo zikwi makumi khumi mphambu zisanu ndi zitatu kudza zana limodzi, monga mwa makamu ao. Iwo ndiwo aziyenda gulu lacitatu paulendo.

Numeri 2

Numeri 2:17-30