Numeri 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Owerengedwa onse a cigono ca Rubeni ndiwo zikwi makumi khumi mphambu makumi asanu ndi cimodzi kudza mazana anai mphambu makumi asanu, monga mwa makamu ao. Ndiwo azitsatana nao otsogolerawo.

Numeri 2

Numeri 2:6-22