Numeri 17:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Pamenepo ana a Israyeli ananena ndi Mose, nati, Taonani, tikufa, tionongeka, tionongeka tonse.

13. Yense wakuyandikiza kacisi wa Yehova amwalira; kodi tidzatha nkufa?

Numeri 17