Numeri 16:49-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

49. Koma akufa nao mliri ndiwo zikwi khumi ndi zinai mphambu mazana asanu ndi awiri, osawerenga aja adafera cija ca Kora.

50. Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la cihema cokomanako; ndi mliri unaleka.

Numeri 16