Numeri 16:43-45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Ndipo Mose ndi Aroni anadza kukhomo kwa cihema cokomanako.

44. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,

45. Kwerani kucoka pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi. Pamenepo adagwa nkhope zao pansi.

Numeri 16