Numeri 16:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, posonkhanidwa khamulo kutsutsana nao Mose ndi Aroni, kuti anaceukira cihema cokomanako; taonani, mtambo unaciphimba, ndi ulemerero wa Yehova unaoneka.

Numeri 16

Numeri 16:41-44