Numeri 16:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mota unaturuka kwa Yehova, ndi kunyeketsa amuna mazana awiri ndi makumi asanu aja akubwera naco cofukiza.

Numeri 16

Numeri 16:33-37