Numeri 16:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco iwowa, ndi onse anali nao, anatsikira kumanda ali ndi moyo, ndi dziko linasunama pa iwo, ndipo anaonongeka pakati pa msonkhano.

Numeri 16

Numeri 16:28-37