Numeri 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mose adapsa mtima, ndipo anati kwa Yehova, Musasamalira copereka cao; siodinalanda buru wao mmodzi, kapena kucitira coipa mmodzi wa iwowa.

Numeri 16

Numeri 16:8-21