Numeri 15:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo uzikonzera nsembe yopsereza kapena yophera, vinyo wa nsembe yothira, limodzi la magawo anai la bini, ukhale wa mwana wa nkhosa mmodzi.

Numeri 15

Numeri 15:1-14