Numeri 15:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kudzatero ndi ng'ombe iri yonse, kapena nkhosa yamphongo iri yonse, kapena mwana wa nkhosa ali yense, kapena mwana wa mbuzi ali yense.

Numeri 15

Numeri 15:8-18