Numeri 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebi mwana wa Yefune, ndiwo a iwo aja adazonda dzikolo, anang'amba zobvala zao;

Numeri 14

Numeri 14:1-7