Numeri 14:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine Yehova ndanena, ndidzacitira ndithu ici khamu ili lonse loipa lakusonkhana kutsutsana nane; adzatha m'cipululu muno, nadzafamo.

Numeri 14

Numeri 14:28-37