Numeri 14:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana anu adzakhala oyendayenda m'cipululu zaka makumi anai, nadzasenza kupulukira kwanu, kufikira mitembo yanu yatha m'cipululu.

Numeri 14

Numeri 14:29-38