Numeri 14:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova atitengeranii kudza nafe kudziko kuno, kuti tigwe nalo lupanga? Akazi athu ndi makanda athu adzakhala cakudya cao; kodi sikuli bwino tibwerere ku Aigupto?

Numeri 14

Numeri 14:1-9