Numeri 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza ku cigwa ca Esikolo, nacekako tsango limodzi la mphesa, nalisenza awiri mopika; anabwera nazonso makangaza ndi nkhuyu.

Numeri 13

Numeri 13:18-29