Numeri 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Tamvani tsono mau anga; pakakhala mneneri pakati pa inu, Ine Yehova ndidzizindikiritsa kwa iye m'masomphenya, ndinena naye m'kulota.

Numeri 12

Numeri 12:5-9