Numeri 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa naco cilakolako; ndi ana a Israyeli omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?

Numeri 11

Numeri 11:3-9