Numeri 11:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose kuyambira ubwana wace, anayankha nati, Mose, mfumu yanga, aletseni.

Numeri 11

Numeri 11:27-35