Numeri 11:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati, Anthu amene ndiri pakati pao, ndiwo zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda pansi, ndipo Inu mwanena, Ndidzawapatsa nyama, kuti adye mwezi wamphumphu.

Numeri 11

Numeri 11:14-24