Numeri 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene mupita kunkhondo m'dziko lanu kucita nkhondo pa mdani wakusautsa inu, mulize cokweza ndi malipenga; ndipo Yehova Mulungu wanu adzakumbukila inu, nadzakupulumutsani kwa adani anu.

Numeri 10

Numeri 10:1-19