Numeri 10:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anati, Usatisiyetu; popeza udziwa poyenera kumanga ife m'cipululu, ndipo udzakhala maso athu.

Numeri 10

Numeri 10:27-34