Numeri 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, caka caciwiri, mwezi waciwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kucokera kwa kacisi wa mboni.

Numeri 10

Numeri 10:8-19