Numeri 1:53-54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

53. Koma Alevi amange mahema ao pozungulira pa kacisi wa mboni, kuti mkwiyo ungagwere khamu la ana a Israyeli; ndipo Alevi azidikira kacisi wa mboni.

54. Momwemo ana a Israyeli anacita monga mwa zonse Yehova adauza Mosel anacita momwemo.

Numeri 1