Numeri 1:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Ndipo maina a amuna amene aime nanu ndi awa: wa Rubeni, Elizuri mwana wa Sedeuri.

6. Wa Simeoni, Selumiyeli mwana wa Zurisadai.

7. Wa Yuda, Nahesoni mwana wa Aminadabu.

Numeri 1