Numeri 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

A ana a Gadi, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akuturukira kunkhondo;

Numeri 1

Numeri 1:20-25