Nehemiya 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaimirira pa ciunda ca Alevi Yesuwa, ndi Bani, Kadimiyeli, Sebaniya, Buni, Serebiya, Bani, ndi Kenani, napfuula ndi mau akuru kwa Yehova Mulungu wao.

Nehemiya 9

Nehemiya 9:1-5