Nehemiya 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anakhala osamvera, napandukira Inu, nataya cilamulo canu m'mbuyo mwao napha aneneri anu akuwacitira umboni, kuwabwezera kwa Inu, nacita zopeputsa zazikuru.

Nehemiya 9

Nehemiya 9:25-29