Nehemiya 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munatsikiranso pa phiri la Sinai, nimunalankhula nao mocokera m'Mwamba, ndipo munawapatsa maweruzo oyenera, ndi cilamulo coona, malemba, ndi malamulo okoma;

Nehemiya 9

Nehemiya 9:4-15