Nehemiya 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Ezara analemekeza Yehova Mulungu wamkuru. Nabvomereza anthu onse, ndi kuti, Amen, Amen; nakweza manja ao, nawerama, nalambira Yehova nkhope zao pansi.

Nehemiya 8

Nehemiya 8:3-9