Nehemiya 8:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ezara wansembe anabwera naco cilamulo pamaso pa msonkhano, ndiwo amuna ndi akazi, ndi yense wakumva ndi kuzindikira tsiku loyamba la mwezi wacisanu ndi ciwiri.

Nehemiya 8

Nehemiya 8:1-7